×

Ndipo tidamupatsa Abrahamu, Isake ndiYakobo ndipo tidakhazikitsa pakati pa ana ake utumiki 29:27 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:27) ayat 27 in Chichewa

29:27 Surah Al-‘Ankabut ayat 27 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 27 - العَنكبُوت - Page - Juz 20

﴿وَوَهَبۡنَا لَهُۥٓ إِسۡحَٰقَ وَيَعۡقُوبَ وَجَعَلۡنَا فِي ذُرِّيَّتِهِ ٱلنُّبُوَّةَ وَٱلۡكِتَٰبَ وَءَاتَيۡنَٰهُ أَجۡرَهُۥ فِي ٱلدُّنۡيَاۖ وَإِنَّهُۥ فِي ٱلۡأٓخِرَةِ لَمِنَ ٱلصَّٰلِحِينَ ﴾
[العَنكبُوت: 27]

Ndipo tidamupatsa Abrahamu, Isake ndiYakobo ndipo tidakhazikitsa pakati pa ana ake utumiki ndi chivumbulutso. Ndipo Ife tidamupatsa mphotho yake m’moyo uno ndipo iye adzakhala m’moyo umene uli nkudza, pagulu la anthu olungama

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ووهبنا له إسحاق ويعقوب وجعلنا في ذريته النبوة والكتاب وآتيناه أجره في, باللغة نيانجا

﴿ووهبنا له إسحاق ويعقوب وجعلنا في ذريته النبوة والكتاب وآتيناه أجره في﴾ [العَنكبُوت: 27]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo tidampatsa (Mneneri Ibrahim) Ishâq ndi Ya’qub, ndipo tidaika uneneri ndi buku pa mbumba yake, ndipo tidampatsa malipiro ake pa dziko lapansi; ndithu iye pa tsiku la chimaliziro adzakhala mwa anthu abwino
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek