×

Iwo amakukakamiza kuti ubweretse chilango msanga. Ndipo zikadakhala kuti nthawi yake siidakhazikitsidwe 29:53 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:53) ayat 53 in Chichewa

29:53 Surah Al-‘Ankabut ayat 53 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 53 - العَنكبُوت - Page - Juz 21

﴿وَيَسۡتَعۡجِلُونَكَ بِٱلۡعَذَابِ وَلَوۡلَآ أَجَلٞ مُّسَمّٗى لَّجَآءَهُمُ ٱلۡعَذَابُۚ وَلَيَأۡتِيَنَّهُم بَغۡتَةٗ وَهُمۡ لَا يَشۡعُرُونَ ﴾
[العَنكبُوت: 53]

Iwo amakukakamiza kuti ubweretse chilango msanga. Ndipo zikadakhala kuti nthawi yake siidakhazikitsidwe kale, ndithudi, chilango chikadakhala chitadza kale pa iwo. Ndithudi icho chidzadza pa iwo mwadzidzidzi pamene iwo sali kuchiganizira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ويستعجلونك بالعذاب ولولا أجل مسمى لجاءهم العذاب وليأتينهم بغتة وهم لا يشعرون, باللغة نيانجا

﴿ويستعجلونك بالعذاب ولولا أجل مسمى لجاءهم العذاب وليأتينهم بغتة وهم لا يشعرون﴾ [العَنكبُوت: 53]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo akukupempha kuti chilango chidze mwachangu; kukadapanda kuti kudaikidwa nthawi yodziwika, chilango chikadawadzera. Ndipo ndithu chidzawadzera mwadzidzidzi asakudziwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek