×

Ndipoiwoameneamakhulupirira ndipo amachita ntchito zabwino, otere tidzawapatsa malo kumwamba amene pansi pake 29:58 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:58) ayat 58 in Chichewa

29:58 Surah Al-‘Ankabut ayat 58 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 58 - العَنكبُوت - Page - Juz 21

﴿وَٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ وَعَمِلُواْ ٱلصَّٰلِحَٰتِ لَنُبَوِّئَنَّهُم مِّنَ ٱلۡجَنَّةِ غُرَفٗا تَجۡرِي مِن تَحۡتِهَا ٱلۡأَنۡهَٰرُ خَٰلِدِينَ فِيهَاۚ نِعۡمَ أَجۡرُ ٱلۡعَٰمِلِينَ ﴾
[العَنكبُوت: 58]

Ndipoiwoameneamakhulupirira ndipo amachita ntchito zabwino, otere tidzawapatsa malo kumwamba amene pansi pake pamayenda mitsinje kuti akhale m’menemo mpaka kale kale. Eti kukoma mphotho ya iwo amene amachita zabwino

❮ Previous Next ❯

ترجمة: والذين آمنوا وعملوا الصالحات لنبوئنهم من الجنة غرفا تجري من تحتها الأنهار, باللغة نيانجا

﴿والذين آمنوا وعملوا الصالحات لنبوئنهم من الجنة غرفا تجري من تحتها الأنهار﴾ [العَنكبُوت: 58]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo amene akhulupirira ndi kumachita zabwino ndithudi tidzawakhazika m’zipinda za ku Munda wamtendere, momwe pansi (ndi patsogolo) pake pakuyenda mitsinje; adzakhala m’menemo nthawi yaitali. Taonani kukhala bwino malipiro a ochita zabwino
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek