Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 6 - العَنكبُوت - Page - Juz 20
﴿وَمَن جَٰهَدَ فَإِنَّمَا يُجَٰهِدُ لِنَفۡسِهِۦٓۚ إِنَّ ٱللَّهَ لَغَنِيٌّ عَنِ ٱلۡعَٰلَمِينَ ﴾
[العَنكبُوت: 6]
﴿ومن جاهد فإنما يجاهد لنفسه إن الله لغني عن العالمين﴾ [العَنكبُوت: 6]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo amene akuchita khama (polimbana ndi Akafiri, kapena pogonjetsa mtima wake kuti utsatire malamulo a Allah), ndithu zabwino za khamalo zili pa iye mwini. Ndithu Allah siwosaukira chilichonse kwa zolengedwa Zake |