×

Ndipo chabwino chilichonse chimene achita, palibe chimene chidzakanidwa chifukwa Mulungu amadziwa anthu 3:115 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah al-‘Imran ⮕ (3:115) ayat 115 in Chichewa

3:115 Surah al-‘Imran ayat 115 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah al-‘Imran ayat 115 - آل عِمران - Page - Juz 4

﴿وَمَا يَفۡعَلُواْ مِنۡ خَيۡرٖ فَلَن يُكۡفَرُوهُۗ وَٱللَّهُ عَلِيمُۢ بِٱلۡمُتَّقِينَ ﴾
[آل عِمران: 115]

Ndipo chabwino chilichonse chimene achita, palibe chimene chidzakanidwa chifukwa Mulungu amadziwa anthu olungama

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وما يفعلوا من خير فلن يكفروه والله عليم بالمتقين, باللغة نيانجا

﴿وما يفعلوا من خير فلن يكفروه والله عليم بالمتقين﴾ [آل عِمران: 115]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo chabwino chilichonse chimene angachite sadzakanidwa nacho, (koma adzawalipira malipiro abwino). Ndipo Allah Ngodziwa za amene akuopa Iye
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek