×

Nena kwa anthu amene sakhulupirira: “Inu mudzagonjetsedwa ndi kusonkhanitsidwa kupita ku Gahena 3:12 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah al-‘Imran ⮕ (3:12) ayat 12 in Chichewa

3:12 Surah al-‘Imran ayat 12 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah al-‘Imran ayat 12 - آل عِمران - Page - Juz 3

﴿قُل لِّلَّذِينَ كَفَرُواْ سَتُغۡلَبُونَ وَتُحۡشَرُونَ إِلَىٰ جَهَنَّمَۖ وَبِئۡسَ ٱلۡمِهَادُ ﴾
[آل عِمران: 12]

Nena kwa anthu amene sakhulupirira: “Inu mudzagonjetsedwa ndi kusonkhanitsidwa kupita ku Gahena omwe ndi malo oipa kukhalako.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل للذين كفروا ستغلبون وتحشرون إلى جهنم وبئس المهاد, باللغة نيانجا

﴿قل للذين كفروا ستغلبون وتحشرون إلى جهنم وبئس المهاد﴾ [آل عِمران: 12]

Khaled Ibrahim Betala
“Auze amene sadakhulupirire: “Posachedwapa mugonjetsedwa ndi kusonkhanitsidwa ndi kuponyedwa ku Moto. Taonani kuipa kwa malo wokakhazikikamo!”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek