×

Kugonjetsedwa kwanu, panthawi imene magulu awiri adakumana, kudalamulidwa ndi Mulungu ndi cholinga 3:166 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah al-‘Imran ⮕ (3:166) ayat 166 in Chichewa

3:166 Surah al-‘Imran ayat 166 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah al-‘Imran ayat 166 - آل عِمران - Page - Juz 4

﴿وَمَآ أَصَٰبَكُمۡ يَوۡمَ ٱلۡتَقَى ٱلۡجَمۡعَانِ فَبِإِذۡنِ ٱللَّهِ وَلِيَعۡلَمَ ٱلۡمُؤۡمِنِينَ ﴾
[آل عِمران: 166]

Kugonjetsedwa kwanu, panthawi imene magulu awiri adakumana, kudalamulidwa ndi Mulungu ndi cholinga chakuti akhoza kuyesa anthu okhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وما أصابكم يوم التقى الجمعان فبإذن الله وليعلم المؤمنين, باللغة نيانجا

﴿وما أصابكم يوم التقى الجمعان فبإذن الله وليعلم المؤمنين﴾ [آل عِمران: 166]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo sautso lomwe lidakupezani tsiku lomwe adakumana magulu awiri ankhondo, lidali mwa chilolezo cha Allah ndikutinso awaonetsere poyera okhulupirira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek