×

Nena: “Ngati inu, ndithudi, mukonda Mulungu, nditsatireni ine. Mulungu adzakukondani ndipo adzakukhululukirani 3:31 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah al-‘Imran ⮕ (3:31) ayat 31 in Chichewa

3:31 Surah al-‘Imran ayat 31 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah al-‘Imran ayat 31 - آل عِمران - Page - Juz 3

﴿قُلۡ إِن كُنتُمۡ تُحِبُّونَ ٱللَّهَ فَٱتَّبِعُونِي يُحۡبِبۡكُمُ ٱللَّهُ وَيَغۡفِرۡ لَكُمۡ ذُنُوبَكُمۡۚ وَٱللَّهُ غَفُورٞ رَّحِيمٞ ﴾
[آل عِمران: 31]

Nena: “Ngati inu, ndithudi, mukonda Mulungu, nditsatireni ine. Mulungu adzakukondani ndipo adzakukhululukirani machimo anu. Mulungu ndi wokhululukira ndi wachisoni chosatha.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل إن كنتم تحبون الله فاتبعوني يحببكم الله ويغفر لكم ذنوبكم والله, باللغة نيانجا

﴿قل إن كنتم تحبون الله فاتبعوني يحببكم الله ويغفر لكم ذنوبكم والله﴾ [آل عِمران: 31]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena: (Iwe Mtumiki) “Ngati inu mukumkonda Allah, tsatani ine; Allah akukondani ndikukukhululukirani machimo anu. Ndipo Allah Ngokhululuka, Ngwachisoni chosatha.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek