×

Nthawi imeneyo Zakariya adapempha kwa Ambuye wake nati: “Ambuye wanga! Ndipatseni ine 3:38 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah al-‘Imran ⮕ (3:38) ayat 38 in Chichewa

3:38 Surah al-‘Imran ayat 38 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah al-‘Imran ayat 38 - آل عِمران - Page - Juz 3

﴿هُنَالِكَ دَعَا زَكَرِيَّا رَبَّهُۥۖ قَالَ رَبِّ هَبۡ لِي مِن لَّدُنكَ ذُرِّيَّةٗ طَيِّبَةًۖ إِنَّكَ سَمِيعُ ٱلدُّعَآءِ ﴾
[آل عِمران: 38]

Nthawi imeneyo Zakariya adapempha kwa Ambuye wake nati: “Ambuye wanga! Ndipatseni ine kuchokera kwa Inu mwana wangwiro. Inu ndithudi mumamva pemphero.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: هنالك دعا زكريا ربه قال رب هب لي من لدنك ذرية طيبة, باللغة نيانجا

﴿هنالك دعا زكريا ربه قال رب هب لي من لدنك ذرية طيبة﴾ [آل عِمران: 38]

Khaled Ibrahim Betala
“Pompo Zakariya adapempha Mbuye wake nati: “Mbuye wanga! Ndipatseni kuchokera kwa Inu mwana wabwino. Ndithudi, Inu ndinu Akumva pempho!”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek