×

Akakhala iwo amene sakhulupirira, Ine ndidzawalanga ndi chilango chowawa m’dziko lino ndi 3:56 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah al-‘Imran ⮕ (3:56) ayat 56 in Chichewa

3:56 Surah al-‘Imran ayat 56 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah al-‘Imran ayat 56 - آل عِمران - Page - Juz 3

﴿فَأَمَّا ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ فَأُعَذِّبُهُمۡ عَذَابٗا شَدِيدٗا فِي ٱلدُّنۡيَا وَٱلۡأٓخِرَةِ وَمَا لَهُم مِّن نَّٰصِرِينَ ﴾
[آل عِمران: 56]

Akakhala iwo amene sakhulupirira, Ine ndidzawalanga ndi chilango chowawa m’dziko lino ndi m’dziko limene lili nkudza ndipo sadzapeza wina wowathandiza

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فأما الذين كفروا فأعذبهم عذابا شديدا في الدنيا والآخرة وما لهم من, باللغة نيانجا

﴿فأما الذين كفروا فأعذبهم عذابا شديدا في الدنيا والآخرة وما لهم من﴾ [آل عِمران: 56]

Khaled Ibrahim Betala
“Tsono amene sadakhulupirire, ndiwakhaulitsa ndi chilango chaukali pa dziko lapansi ndi tsiku lachimaliziro, ndipo sadzapeza athandizi
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek