×

Akakhala iwo amene ndi okhulupirira ndipo amachita ntchito zabwino, Mulungu adzawalipira mphotho 3:57 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah al-‘Imran ⮕ (3:57) ayat 57 in Chichewa

3:57 Surah al-‘Imran ayat 57 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah al-‘Imran ayat 57 - آل عِمران - Page - Juz 3

﴿وَأَمَّا ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ وَعَمِلُواْ ٱلصَّٰلِحَٰتِ فَيُوَفِّيهِمۡ أُجُورَهُمۡۗ وَٱللَّهُ لَا يُحِبُّ ٱلظَّٰلِمِينَ ﴾
[آل عِمران: 57]

Akakhala iwo amene ndi okhulupirira ndipo amachita ntchito zabwino, Mulungu adzawalipira mphotho yawo yokwanira. Ndipo Mulungu sakonda anthu ochita zoipa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وأما الذين آمنوا وعملوا الصالحات فيوفيهم أجورهم والله لا يحب الظالمين, باللغة نيانجا

﴿وأما الذين آمنوا وعملوا الصالحات فيوفيهم أجورهم والله لا يحب الظالمين﴾ [آل عِمران: 57]

Khaled Ibrahim Betala
“Koma amene akhulupirira nachita zabwino, (Allah) adzawalipira malipiro awo (mokwanira). Ndipo Allah sakonda anthu ochita zoipa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek