×

Ena mwa anthu amene amakhulupirira Buku amafuna kukusocheretsa iwe. Komatu iwo sangasocheretse 3:69 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah al-‘Imran ⮕ (3:69) ayat 69 in Chichewa

3:69 Surah al-‘Imran ayat 69 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah al-‘Imran ayat 69 - آل عِمران - Page - Juz 3

﴿وَدَّت طَّآئِفَةٞ مِّنۡ أَهۡلِ ٱلۡكِتَٰبِ لَوۡ يُضِلُّونَكُمۡ وَمَا يُضِلُّونَ إِلَّآ أَنفُسَهُمۡ وَمَا يَشۡعُرُونَ ﴾
[آل عِمران: 69]

Ena mwa anthu amene amakhulupirira Buku amafuna kukusocheretsa iwe. Komatu iwo sangasocheretse wina aliyense koma iwo eni, ndipo iwo sazindikira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ودت طائفة من أهل الكتاب لو يضلونكم وما يضلون إلا أنفسهم وما, باللغة نيانجا

﴿ودت طائفة من أهل الكتاب لو يضلونكم وما يضلون إلا أنفسهم وما﴾ [آل عِمران: 69]

Khaled Ibrahim Betala
“Gulu lina la anthu amene adapatsidwa buku likufuna kukusokeretsani; ndipo sasokeretsa aliyense koma iwo wokha, pomwe (iwo eni) sakuzindikira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek