Quran with Chichewa translation - Surah al-‘Imran ayat 96 - آل عِمران - Page - Juz 4
﴿إِنَّ أَوَّلَ بَيۡتٖ وُضِعَ لِلنَّاسِ لَلَّذِي بِبَكَّةَ مُبَارَكٗا وَهُدٗى لِّلۡعَٰلَمِينَ ﴾
[آل عِمران: 96]
﴿إن أول بيت وضع للناس للذي ببكة مباركا وهدى للعالمين﴾ [آل عِمران: 96]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithudi, nyumba yoyamba yomwe idakhazikitsidwa chifukwa cha anthu (kuti azipempheramo) ndiyomwe ili pa Bakka (ku Makka); yodalitsidwa ndiponso ndichiongolo kwa anthu onse |