Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Rum ayat 11 - الرُّوم - Page - Juz 21
﴿ٱللَّهُ يَبۡدَؤُاْ ٱلۡخَلۡقَ ثُمَّ يُعِيدُهُۥ ثُمَّ إِلَيۡهِ تُرۡجَعُونَ ﴾
[الرُّوم: 11]
﴿الله يبدأ الخلق ثم يعيده ثم إليه ترجعون﴾ [الرُّوم: 11]
Khaled Ibrahim Betala “Allah amayambitsa kulenga (zolengedwa), kenako adzabwerezanso (kulengako pambuyo pa imfa yawo), kenako mudzabwezedwa kwa Iye (kuti mudzaweruzidwe) |