×

Ndipo iwe siungathe kumutsogolera munthu wakhungu kuti asiye kulakwa kwake. Palibe amene 30:53 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ar-Rum ⮕ (30:53) ayat 53 in Chichewa

30:53 Surah Ar-Rum ayat 53 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Rum ayat 53 - الرُّوم - Page - Juz 21

﴿وَمَآ أَنتَ بِهَٰدِ ٱلۡعُمۡيِ عَن ضَلَٰلَتِهِمۡۖ إِن تُسۡمِعُ إِلَّا مَن يُؤۡمِنُ بِـَٔايَٰتِنَا فَهُم مُّسۡلِمُونَ ﴾
[الرُّوم: 53]

Ndipo iwe siungathe kumutsogolera munthu wakhungu kuti asiye kulakwa kwake. Palibe amene adzakumvera kupatula okhawo amene amakhulupirira mu chiphunzitso chathu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وما أنت بهاد العمي عن ضلالتهم إن تسمع إلا من يؤمن بآياتنا, باللغة نيانجا

﴿وما أنت بهاد العمي عن ضلالتهم إن تسمع إلا من يؤمن بآياتنا﴾ [الرُّوم: 53]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo iwe sungathe kuwaongolera akhungu m’kusokera kwawo. Sungachititse kuti amve koma okhawo amene akhulupirira Ayah Zathu. Iwowo ndiwo odzipereka
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek