×

Kotero pirirani. Lonjezo la Mulungu ndi loona ndipo usalole anthu opanda chikhulupiriro 30:60 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ar-Rum ⮕ (30:60) ayat 60 in Chichewa

30:60 Surah Ar-Rum ayat 60 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Rum ayat 60 - الرُّوم - Page - Juz 21

﴿فَٱصۡبِرۡ إِنَّ وَعۡدَ ٱللَّهِ حَقّٞۖ وَلَا يَسۡتَخِفَّنَّكَ ٱلَّذِينَ لَا يُوقِنُونَ ﴾
[الرُّوم: 60]

Kotero pirirani. Lonjezo la Mulungu ndi loona ndipo usalole anthu opanda chikhulupiriro kuti akuderere iwe

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فاصبر إن وعد الله حق ولا يستخفنك الذين لا يوقنون, باللغة نيانجا

﴿فاصبر إن وعد الله حق ولا يستخفنك الذين لا يوقنون﴾ [الرُّوم: 60]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho pirira (iwe Mtumiki ku masautso awo). Ndithu lonjezo la Allah, nloona, ndipo asakugwetse mphwayi amene alibe chikhulupiriro chotsimikizika
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek