×

Kalengedwe kanu ndi kuukitsidwa kwanu kwa akufa si chinthu chovuta ayi. Ndithudi 31:28 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Luqman ⮕ (31:28) ayat 28 in Chichewa

31:28 Surah Luqman ayat 28 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Luqman ayat 28 - لُقمَان - Page - Juz 21

﴿مَّا خَلۡقُكُمۡ وَلَا بَعۡثُكُمۡ إِلَّا كَنَفۡسٖ وَٰحِدَةٍۚ إِنَّ ٱللَّهَ سَمِيعُۢ بَصِيرٌ ﴾
[لُقمَان: 28]

Kalengedwe kanu ndi kuukitsidwa kwanu kwa akufa si chinthu chovuta ayi. Ndithudi Mulungu ndi wakumva ndi wowona

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ما خلقكم ولا بعثكم إلا كنفس واحدة إن الله سميع بصير, باللغة نيانجا

﴿ما خلقكم ولا بعثكم إلا كنفس واحدة إن الله سميع بصير﴾ [لُقمَان: 28]

Khaled Ibrahim Betala
“Kulengedwa kwanu, ngakhale kuukitsidwa kwanu m’manda sikuli kanthu koma kuli ngati (kulenga kapena kuukitsa kwa) munthu mmodzi. (Palibe chokanika kwa Allah). Ndithu Allah Ngwakumva, Ngopenya chilichonse
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek