×

Kodi wolakwa kwambiri ndani kuposa munthu amene amati akakumbutsidwa chiphunzitso cha Ambuye 32:22 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah As-Sajdah ⮕ (32:22) ayat 22 in Chichewa

32:22 Surah As-Sajdah ayat 22 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah As-Sajdah ayat 22 - السَّجدة - Page - Juz 21

﴿وَمَنۡ أَظۡلَمُ مِمَّن ذُكِّرَ بِـَٔايَٰتِ رَبِّهِۦ ثُمَّ أَعۡرَضَ عَنۡهَآۚ إِنَّا مِنَ ٱلۡمُجۡرِمِينَ مُنتَقِمُونَ ﴾
[السَّجدة: 22]

Kodi wolakwa kwambiri ndani kuposa munthu amene amati akakumbutsidwa chiphunzitso cha Ambuye wake, iye amabwerera m’mbuyo? Ndithudi Ife tidzalanga anthu ochimwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ومن أظلم ممن ذكر بآيات ربه ثم أعرض عنها إنا من المجرمين, باللغة نيانجا

﴿ومن أظلم ممن ذكر بآيات ربه ثم أعرض عنها إنا من المجرمين﴾ [السَّجدة: 22]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi ndani wachinyengo kwambiri, woposa yemwe akukumbutsidwa Ayah za Mbuye wake, kenako nkuzikana? Ndithu Ife, tidzawabwezera zoipa anthu oipa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek