×

Nena, “Kodi ndani amene angakutetezeni inu kwa Mulungu ngati iye atafuna kuti 33:17 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahzab ⮕ (33:17) ayat 17 in Chichewa

33:17 Surah Al-Ahzab ayat 17 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 17 - الأحزَاب - Page - Juz 21

﴿قُلۡ مَن ذَا ٱلَّذِي يَعۡصِمُكُم مِّنَ ٱللَّهِ إِنۡ أَرَادَ بِكُمۡ سُوٓءًا أَوۡ أَرَادَ بِكُمۡ رَحۡمَةٗۚ وَلَا يَجِدُونَ لَهُم مِّن دُونِ ٱللَّهِ وَلِيّٗا وَلَا نَصِيرٗا ﴾
[الأحزَاب: 17]

Nena, “Kodi ndani amene angakutetezeni inu kwa Mulungu ngati iye atafuna kuti akulangeni inu? Kodi ndani amene akhoza kumuletsa Mulungu ngati atafuna kuti akuonetseni chifundo chake?” Ndipo iwo sadzapeza wina kupatula Mulungu kukhala mtetezi kapena mthandizi wawo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل من ذا الذي يعصمكم من الله إن أراد بكم سوءا أو, باللغة نيانجا

﴿قل من ذا الذي يعصمكم من الله إن أراد بكم سوءا أو﴾ [الأحزَاب: 17]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena: “Kodi ndani amene angakutetezeni kwa Allah, ngati atafuna kukuchitirani choipa; kapena atafuna kukuchitirani chifundo?” Ndipo sadzapeza mthandizi ndi mtetezi kupatula Allah
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek