×

Nena, “Kuthawa sikudzakuthandizani inu ngati inu muli kuthawa imfa, kapena kuphedwa. Ndipo 33:16 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahzab ⮕ (33:16) ayat 16 in Chichewa

33:16 Surah Al-Ahzab ayat 16 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 16 - الأحزَاب - Page - Juz 21

﴿قُل لَّن يَنفَعَكُمُ ٱلۡفِرَارُ إِن فَرَرۡتُم مِّنَ ٱلۡمَوۡتِ أَوِ ٱلۡقَتۡلِ وَإِذٗا لَّا تُمَتَّعُونَ إِلَّا قَلِيلٗا ﴾
[الأحزَاب: 16]

Nena, “Kuthawa sikudzakuthandizani inu ngati inu muli kuthawa imfa, kapena kuphedwa. Ndipo ngakhale kuti inu mungathawe, mudzangosangalala m’moyo wa pa dziko lino lapansi pa kanthawi kochepa chabe.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل لن ينفعكم الفرار إن فررتم من الموت أو القتل وإذا لا, باللغة نيانجا

﴿قل لن ينفعكم الفرار إن فررتم من الموت أو القتل وإذا لا﴾ [الأحزَاب: 16]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena: “Kuthawa sikungakuthandizeni ngati mukuthawa imfa kapena kuphedwa; choncho (kuthawa kwanuku) simusangalatsidwa (nako) koma pang’ono basi. (Kenako ikatha nthawi ya moyo wanu, mukufa).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek