×

Ndipo ngati inu mufuna Mulungu ndi Mtumwi wake ndi moyo umene uli 33:29 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahzab ⮕ (33:29) ayat 29 in Chichewa

33:29 Surah Al-Ahzab ayat 29 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 29 - الأحزَاب - Page - Juz 21

﴿وَإِن كُنتُنَّ تُرِدۡنَ ٱللَّهَ وَرَسُولَهُۥ وَٱلدَّارَ ٱلۡأٓخِرَةَ فَإِنَّ ٱللَّهَ أَعَدَّ لِلۡمُحۡسِنَٰتِ مِنكُنَّ أَجۡرًا عَظِيمٗا ﴾
[الأحزَاب: 29]

Ndipo ngati inu mufuna Mulungu ndi Mtumwi wake ndi moyo umene uli nkudza, ndithudi, Mulungu wawakonzera mphotho yaikulu anthu ochita zabwino amene ali pakati panu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإن كنتن تردن الله ورسوله والدار الآخرة فإن الله أعد للمحسنات منكن, باللغة نيانجا

﴿وإن كنتن تردن الله ورسوله والدار الآخرة فإن الله أعد للمحسنات منكن﴾ [الأحزَاب: 29]

Khaled Ibrahim Betala
““Ndipo ngati mukufuna Allah ndi Mtumiki Wake, ndi nyumba yomaliza, ndithu Allah wawakonzera ochita zabwino mwa inu malipiro aakulu.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek