×

Oh inu anthu okhulupirira! Pamene mukwatira akazi okhulupirira ndipo muwasudzula musanalowane nawo, 33:49 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahzab ⮕ (33:49) ayat 49 in Chichewa

33:49 Surah Al-Ahzab ayat 49 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 49 - الأحزَاب - Page - Juz 22

﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلَّذِينَ ءَامَنُوٓاْ إِذَا نَكَحۡتُمُ ٱلۡمُؤۡمِنَٰتِ ثُمَّ طَلَّقۡتُمُوهُنَّ مِن قَبۡلِ أَن تَمَسُّوهُنَّ فَمَا لَكُمۡ عَلَيۡهِنَّ مِنۡ عِدَّةٖ تَعۡتَدُّونَهَاۖ فَمَتِّعُوهُنَّ وَسَرِّحُوهُنَّ سَرَاحٗا جَمِيلٗا ﴾
[الأحزَاب: 49]

Oh inu anthu okhulupirira! Pamene mukwatira akazi okhulupirira ndipo muwasudzula musanalowane nawo, palibe nthawi yoyembekezera pakhomo panu. Kotero asanachoke apatseni mphatso yawo ndipo alekeni kuti achoke mwaubwino

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياأيها الذين آمنوا إذا نكحتم المؤمنات ثم طلقتموهن من قبل أن تمسوهن, باللغة نيانجا

﴿ياأيها الذين آمنوا إذا نكحتم المؤمنات ثم طلقتموهن من قبل أن تمسوهن﴾ [الأحزَاب: 49]

Khaled Ibrahim Betala
“E inu amene mwakhulupirira! Mukakwatira akazi okhulupirira, kenako ndikulekana nawo musadawakhudze, inu mulibe chiwerengero cha ‘Edda’ pa iwo choti nkuchiwerengera. Asangalatseni powapatsa cholekanira. siyananawoni; kusiyana kwabwino
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek