Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 8 - الأحزَاب - Page - Juz 21
﴿لِّيَسۡـَٔلَ ٱلصَّٰدِقِينَ عَن صِدۡقِهِمۡۚ وَأَعَدَّ لِلۡكَٰفِرِينَ عَذَابًا أَلِيمٗا ﴾
[الأحزَاب: 8]
﴿ليسأل الصادقين عن صدقهم وأعد للكافرين عذابا أليما﴾ [الأحزَاب: 8]
Khaled Ibrahim Betala “Kuti (Allah) adzafunse owona (aneneri) (tsiku la chimaliziro) pa zimene adanena (kwa anthu awo zakufikitsa uthenga woonadi kwa iwo). Ndipo Allah wawakonzera (osakhulupirira) chilango chopweteka |