Quran with Chichewa translation - Surah Saba’ ayat 50 - سَبإ - Page - Juz 22
﴿قُلۡ إِن ضَلَلۡتُ فَإِنَّمَآ أَضِلُّ عَلَىٰ نَفۡسِيۖ وَإِنِ ٱهۡتَدَيۡتُ فَبِمَا يُوحِيٓ إِلَيَّ رَبِّيٓۚ إِنَّهُۥ سَمِيعٞ قَرِيبٞ ﴾
[سَبإ: 50]
﴿قل إن ضللت فإنما أضل على نفسي وإن اهتديت فبما يوحي إلي﴾ [سَبإ: 50]
Khaled Ibrahim Betala “Nena: “Ngati ndasokera, ndiye kuti ndadzisokeretsa ndekha (ndadziyika ndekha m’mavuto). Koma ngati ndaongoka, ndichifukwa cha zimene akundivumbulutsira Mbuye wanga. Ndithu Iye Ngwakumva; ali pafupi (ndi aliyense).” |