Quran with Chichewa translation - Surah Saba’ ayat 6 - سَبإ - Page - Juz 22
﴿وَيَرَى ٱلَّذِينَ أُوتُواْ ٱلۡعِلۡمَ ٱلَّذِيٓ أُنزِلَ إِلَيۡكَ مِن رَّبِّكَ هُوَ ٱلۡحَقَّ وَيَهۡدِيٓ إِلَىٰ صِرَٰطِ ٱلۡعَزِيزِ ٱلۡحَمِيدِ ﴾
[سَبإ: 6]
﴿ويرى الذين أوتوا العلم الذي أنـزل إليك من ربك هو الحق ويهدي﴾ [سَبإ: 6]
Khaled Ibrahim Betala “Koma amene apatsidwa (dalitso la) kudziwa akuzindikira kuti zimene zavumbulutsidwa kwa iwe kuchokera kwa Mbuye wako nzoona, ndipo zikuongolera ku njira ya Mwini mphamvu zoposa, Wotamandidwa |