Quran with Chichewa translation - Surah Saba’ ayat 8 - سَبإ - Page - Juz 22
﴿أَفۡتَرَىٰ عَلَى ٱللَّهِ كَذِبًا أَم بِهِۦ جِنَّةُۢۗ بَلِ ٱلَّذِينَ لَا يُؤۡمِنُونَ بِٱلۡأٓخِرَةِ فِي ٱلۡعَذَابِ وَٱلضَّلَٰلِ ٱلۡبَعِيدِ ﴾
[سَبإ: 8]
﴿أفترى على الله كذبا أم به جنة بل الذين لا يؤمنون بالآخرة﴾ [سَبإ: 8]
Khaled Ibrahim Betala “(Allah akunena): “Kodi (akum’ganizira Muhammad kuti) wamupekera Allah bodza, kapena wagwidwa ndi misala? Iyayi, koma osakhulupirira za tsiku la chimaliziro adzakhala m’chilango ndi m’kusokera kwakukulu.” |