Quran with Chichewa translation - Surah Saba’ ayat 9 - سَبإ - Page - Juz 22
﴿أَفَلَمۡ يَرَوۡاْ إِلَىٰ مَا بَيۡنَ أَيۡدِيهِمۡ وَمَا خَلۡفَهُم مِّنَ ٱلسَّمَآءِ وَٱلۡأَرۡضِۚ إِن نَّشَأۡ نَخۡسِفۡ بِهِمُ ٱلۡأَرۡضَ أَوۡ نُسۡقِطۡ عَلَيۡهِمۡ كِسَفٗا مِّنَ ٱلسَّمَآءِۚ إِنَّ فِي ذَٰلِكَ لَأٓيَةٗ لِّكُلِّ عَبۡدٖ مُّنِيبٖ ﴾
[سَبإ: 9]
﴿أفلم يروا إلى ما بين أيديهم وما خلفهم من السماء والأرض إن﴾ [سَبإ: 9]
Khaled Ibrahim Betala “Kodi (agwidwa ndi khungu) saona zomwe zili patsogolo pawo ndi pambuyo pawo monga thambo ndi nthaka (kuti adziwe kukhoza Kwathu kuchita zimene tafuna)? Tikadafuna tikadawakwilira ndi nthaka kapena kuwagwetsera zidutswa za thambo. Ndithu m’zimenezo muli malingaliro kwa kapolo aliyense wotembenukira (kwa Allah) |