Quran with Chichewa translation - Surah FaTir ayat 22 - فَاطِر - Page - Juz 22
﴿وَمَا يَسۡتَوِي ٱلۡأَحۡيَآءُ وَلَا ٱلۡأَمۡوَٰتُۚ إِنَّ ٱللَّهَ يُسۡمِعُ مَن يَشَآءُۖ وَمَآ أَنتَ بِمُسۡمِعٖ مَّن فِي ٱلۡقُبُورِ ﴾
[فَاطِر: 22]
﴿وما يستوي الأحياء ولا الأموات إن الله يسمع من يشاء وما أنت﴾ [فَاطِر: 22]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo amoyo ndi akufa safanana (amene mitima yawo ili ndi moyo pokhala ndi chikhulupiliro, ndi amene mitima yawo ili yakufa posakhala ndi chikhulupiliro, ngosafanana). Ndithu Allah akumumveretsa amene wam’funa; koma iwe sungathe kumumveretsa amene ali m’manda |