Quran with Chichewa translation - Surah FaTir ayat 30 - فَاطِر - Page - Juz 22
﴿لِيُوَفِّيَهُمۡ أُجُورَهُمۡ وَيَزِيدَهُم مِّن فَضۡلِهِۦٓۚ إِنَّهُۥ غَفُورٞ شَكُورٞ ﴾
[فَاطِر: 30]
﴿ليوفيهم أجورهم ويزيدهم من فضله إنه غفور شكور﴾ [فَاطِر: 30]
Khaled Ibrahim Betala “Kuti akawakwaniritsire malipiro awo ndi kuwaonjezera zabwino Zake; ndithu Iye Ngokhululuka kwabasi; Ngothokoza kwambiri |