×

Iwo amene amawerenga Buku la Mulungu, amene amapitiriza kupemphera nthawi zonse ndipo 35:29 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah FaTir ⮕ (35:29) ayat 29 in Chichewa

35:29 Surah FaTir ayat 29 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah FaTir ayat 29 - فَاطِر - Page - Juz 22

﴿إِنَّ ٱلَّذِينَ يَتۡلُونَ كِتَٰبَ ٱللَّهِ وَأَقَامُواْ ٱلصَّلَوٰةَ وَأَنفَقُواْ مِمَّا رَزَقۡنَٰهُمۡ سِرّٗا وَعَلَانِيَةٗ يَرۡجُونَ تِجَٰرَةٗ لَّن تَبُورَ ﴾
[فَاطِر: 29]

Iwo amene amawerenga Buku la Mulungu, amene amapitiriza kupemphera nthawi zonse ndipo amapereka chaulere pa katundu amene tawapatsa mwamseri kapena poyera, ayenera kukhulupirira m’malonda amene sadzatha ayi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن الذين يتلون كتاب الله وأقاموا الصلاة وأنفقوا مما رزقناهم سرا وعلانية, باللغة نيانجا

﴿إن الذين يتلون كتاب الله وأقاموا الصلاة وأنفقوا مما رزقناهم سرا وعلانية﴾ [فَاطِر: 29]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu amene akuwerenga buku la Allah uku nkumapemphera Swala moyenera napereka m’zimene tawapatsa mwanseri ndi moonetsera, iwo akuyembekezera malonda osaonongeka
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek