×

Ndipo chimene tavumbulutsa kwa iwe kuchokera m’Buku ndi choonadi chimene chitsimikiza zimene 35:31 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah FaTir ⮕ (35:31) ayat 31 in Chichewa

35:31 Surah FaTir ayat 31 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah FaTir ayat 31 - فَاطِر - Page - Juz 22

﴿وَٱلَّذِيٓ أَوۡحَيۡنَآ إِلَيۡكَ مِنَ ٱلۡكِتَٰبِ هُوَ ٱلۡحَقُّ مُصَدِّقٗا لِّمَا بَيۡنَ يَدَيۡهِۗ إِنَّ ٱللَّهَ بِعِبَادِهِۦ لَخَبِيرُۢ بَصِيرٞ ﴾
[فَاطِر: 31]

Ndipo chimene tavumbulutsa kwa iwe kuchokera m’Buku ndi choonadi chimene chitsimikiza zimene zidalipo kale. Ndithudi Mulungu amadziwa ndipo amaona zochita za akapolo ake

❮ Previous Next ❯

ترجمة: والذي أوحينا إليك من الكتاب هو الحق مصدقا لما بين يديه إن, باللغة نيانجا

﴿والذي أوحينا إليك من الكتاب هو الحق مصدقا لما بين يديه إن﴾ [فَاطِر: 31]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo buku limene takuvumbulutsira, nloona; likutsimikizira za mabuku omwe adali patsogolo pake. Ndithu Allah kwa akapolo Ake Ngodziwa kwambiri ndiponso akuwaona bwino
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek