×

Ndipoiwoadzati,“Kuyamikidwakonsendikwa Mulungu amene wachotsa chisoni pakati pathu. Ndithudi Ambuye wathu ndi wokhululukira 35:34 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah FaTir ⮕ (35:34) ayat 34 in Chichewa

35:34 Surah FaTir ayat 34 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah FaTir ayat 34 - فَاطِر - Page - Juz 22

﴿وَقَالُواْ ٱلۡحَمۡدُ لِلَّهِ ٱلَّذِيٓ أَذۡهَبَ عَنَّا ٱلۡحَزَنَۖ إِنَّ رَبَّنَا لَغَفُورٞ شَكُورٌ ﴾
[فَاطِر: 34]

Ndipoiwoadzati,“Kuyamikidwakonsendikwa Mulungu amene wachotsa chisoni pakati pathu. Ndithudi Ambuye wathu ndi wokhululukira ndiponso amene amachulukitsa malipiro.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقالوا الحمد لله الذي أذهب عنا الحزن إن ربنا لغفور شكور, باللغة نيانجا

﴿وقالوا الحمد لله الذي أذهب عنا الحزن إن ربنا لغفور شكور﴾ [فَاطِر: 34]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo adzanena (pakuthokoza kwawo): “Kutamandidwa konse nkwa Allah Amene watichotsera madandaulo; ndithu Mbuye wathu Ngokhululuka kwambiri, Ngothokoza kwabasi.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek