×

Iwo adzalowa m’minda yokhalitsa ndipo azidzavala zibangiri zagolide ndi nkhombe ndipo zovala 35:33 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah FaTir ⮕ (35:33) ayat 33 in Chichewa

35:33 Surah FaTir ayat 33 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah FaTir ayat 33 - فَاطِر - Page - Juz 22

﴿جَنَّٰتُ عَدۡنٖ يَدۡخُلُونَهَا يُحَلَّوۡنَ فِيهَا مِنۡ أَسَاوِرَ مِن ذَهَبٖ وَلُؤۡلُؤٗاۖ وَلِبَاسُهُمۡ فِيهَا حَرِيرٞ ﴾
[فَاطِر: 33]

Iwo adzalowa m’minda yokhalitsa ndipo azidzavala zibangiri zagolide ndi nkhombe ndipo zovala zawo zidzakhala za silika

❮ Previous Next ❯

ترجمة: جنات عدن يدخلونها يحلون فيها من أساور من ذهب ولؤلؤا ولباسهم فيها, باللغة نيانجا

﴿جنات عدن يدخلونها يحلون فيها من أساور من ذهب ولؤلؤا ولباسهم فيها﴾ [فَاطِر: 33]

Khaled Ibrahim Betala
“Adzailowa minda yamuyaya; m’menemo adzakongoletsedwa povekedwa zibangiri zagolide ndi ngale; nsalu ya silika ndicho chovala chawo m’menemo
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek