×

Ndithudi Mulungu amadziwa zonse zobisika zakumwamba ndi pa dziko lapansi. Ndithudi Iye 35:38 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah FaTir ⮕ (35:38) ayat 38 in Chichewa

35:38 Surah FaTir ayat 38 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah FaTir ayat 38 - فَاطِر - Page - Juz 22

﴿إِنَّ ٱللَّهَ عَٰلِمُ غَيۡبِ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِۚ إِنَّهُۥ عَلِيمُۢ بِذَاتِ ٱلصُّدُورِ ﴾
[فَاطِر: 38]

Ndithudi Mulungu amadziwa zonse zobisika zakumwamba ndi pa dziko lapansi. Ndithudi Iye amaona zimene zili m’mitima mwa anthu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن الله عالم غيب السموات والأرض إنه عليم بذات الصدور, باللغة نيانجا

﴿إن الله عالم غيب السموات والأرض إنه عليم بذات الصدور﴾ [فَاطِر: 38]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu Allah Ngodziwa zobisika za kumwamba ndi za pansi. Iye Ngodziwa kwambiri za m’zifuwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek