Quran with Chichewa translation - Surah FaTir ayat 8 - فَاطِر - Page - Juz 22
﴿أَفَمَن زُيِّنَ لَهُۥ سُوٓءُ عَمَلِهِۦ فَرَءَاهُ حَسَنٗاۖ فَإِنَّ ٱللَّهَ يُضِلُّ مَن يَشَآءُ وَيَهۡدِي مَن يَشَآءُۖ فَلَا تَذۡهَبۡ نَفۡسُكَ عَلَيۡهِمۡ حَسَرَٰتٍۚ إِنَّ ٱللَّهَ عَلِيمُۢ بِمَا يَصۡنَعُونَ ﴾
[فَاطِر: 8]
﴿أفمن زين له سوء عمله فرآه حسنا فإن الله يضل من يشاء﴾ [فَاطِر: 8]
Khaled Ibrahim Betala “Kodi amene zochita zake zoipa zakometsedwa kwa iye nkumaziona kuti nzabwino, (ngolingana ndi amene waongoka ndi chiongoko cha Allah kotero kuti chabwino nkuchiyesa chabwino; choipa nkuchiyesa choipa?) Ndithu Allah akumlekelera kuti asokere yemwe wamfuna (chifukwa chakuti safuna kuongoka), ndipo akuongola amene wam’funa. Choncho moyo wako usaonongeke chifukwa chowadandaula iwo. Ndithu Allah Ngodziwa zonse zimene (iwo) akuchita |