Quran with Chichewa translation - Surah FaTir ayat 9 - فَاطِر - Page - Juz 22
﴿وَٱللَّهُ ٱلَّذِيٓ أَرۡسَلَ ٱلرِّيَٰحَ فَتُثِيرُ سَحَابٗا فَسُقۡنَٰهُ إِلَىٰ بَلَدٖ مَّيِّتٖ فَأَحۡيَيۡنَا بِهِ ٱلۡأَرۡضَ بَعۡدَ مَوۡتِهَاۚ كَذَٰلِكَ ٱلنُّشُورُ ﴾
[فَاطِر: 9]
﴿والله الذي أرسل الرياح فتثير سحابا فسقناه إلى بلد ميت فأحيينا به﴾ [فَاطِر: 9]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo Allah ndiamene amatumiza mphepo; choncho imagwedeza mitambo (ya mvula) ndipo timaifikitsa ku dziko lakufa. Ndipo kupyolera m’madzi otuluka mmitamboyo; timaiwukitsa nthaka pambuyo pakufa kwake, momwemonso ndimmene kudzakhalira kutuluka akufa (m’manda tsiku la chiweruziro) |