Quran with Chichewa translation - Surah Ya-Sin ayat 27 - يسٓ - Page - Juz 23
﴿بِمَا غَفَرَ لِي رَبِّي وَجَعَلَنِي مِنَ ٱلۡمُكۡرَمِينَ ﴾
[يسٓ: 27]
﴿بما غفر لي ربي وجعلني من المكرمين﴾ [يسٓ: 27]
Khaled Ibrahim Betala ““Momwe Mbuye wanga wandikhululukira ndikundichita kukhala mmodzi wa opatsidwa ulemu (akadakhulupirira).” |