Quran with Chichewa translation - Surah Ya-Sin ayat 28 - يسٓ - Page - Juz 23
﴿۞ وَمَآ أَنزَلۡنَا عَلَىٰ قَوۡمِهِۦ مِنۢ بَعۡدِهِۦ مِن جُندٖ مِّنَ ٱلسَّمَآءِ وَمَا كُنَّا مُنزِلِينَ ﴾
[يسٓ: 28]
﴿وما أنـزلنا على قومه من بعده من جند من السماء وما كنا﴾ [يسٓ: 28]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo anthu ake sitidawatsitsire ankhondo ochokera kumwamba pambuyo pake (kuti awaononge). Ndipo pachizolowezi chathu sititsitsa (ankhondo kumwamba tikafuna kuononga, koma Mngelo mmodzi amakwanira) |