Quran with Chichewa translation - Surah Ya-Sin ayat 41 - يسٓ - Page - Juz 23
﴿وَءَايَةٞ لَّهُمۡ أَنَّا حَمَلۡنَا ذُرِّيَّتَهُمۡ فِي ٱلۡفُلۡكِ ٱلۡمَشۡحُونِ ﴾
[يسٓ: 41]
﴿وآية لهم أنا حملنا ذريتهم في الفلك المشحون﴾ [يسٓ: 41]
Khaled Ibrahim Betala “Ndiponso pali chisonyezo kwa iwo (chosonyeza madalitso Athu pa iwo). Ndithu tidaukweza mtundu wawo mchombo chodzazidwa (ndi zonse zamoyo) |