Quran with Chichewa translation - Surah Ya-Sin ayat 40 - يسٓ - Page - Juz 23
﴿لَا ٱلشَّمۡسُ يَنۢبَغِي لَهَآ أَن تُدۡرِكَ ٱلۡقَمَرَ وَلَا ٱلَّيۡلُ سَابِقُ ٱلنَّهَارِۚ وَكُلّٞ فِي فَلَكٖ يَسۡبَحُونَ ﴾
[يسٓ: 40]
﴿لا الشمس ينبغي لها أن تدرك القمر ولا الليل سابق النهار وكل﴾ [يسٓ: 40]
Khaled Ibrahim Betala “Nkosatheka kwa dzuwa kukumana ndi mwezi (njira yake); nawonso usiku sungathe kupambana usana (pakudza nthawi yausana isadathe, koma zimasinthana). Ndipo chilichonse mwa izo chimasambira m’njira yake (imene Allah adachikonzera) |