Quran with Chichewa translation - Surah Ya-Sin ayat 46 - يسٓ - Page - Juz 23
﴿وَمَا تَأۡتِيهِم مِّنۡ ءَايَةٖ مِّنۡ ءَايَٰتِ رَبِّهِمۡ إِلَّا كَانُواْ عَنۡهَا مُعۡرِضِينَ ﴾
[يسٓ: 46]
﴿وما تأتيهم من آية من آيات ربهم إلا كانوا عنها معرضين﴾ [يسٓ: 46]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo palibe chisonyezo chilichonse mwa zisonyezo za Mbuye wawo (zosonyeza umodzi Wake ndi kukhoza Kwake) chomwe chidawadzera popanda kuchinyoza (ndi kuchikana) |