×

Pamene zinenedwa kwa iwo kuti, “Opani chinthu chimene chili patsogolo panu ndi 36:45 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ya-Sin ⮕ (36:45) ayat 45 in Chichewa

36:45 Surah Ya-Sin ayat 45 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ya-Sin ayat 45 - يسٓ - Page - Juz 23

﴿وَإِذَا قِيلَ لَهُمُ ٱتَّقُواْ مَا بَيۡنَ أَيۡدِيكُمۡ وَمَا خَلۡفَكُمۡ لَعَلَّكُمۡ تُرۡحَمُونَ ﴾
[يسٓ: 45]

Pamene zinenedwa kwa iwo kuti, “Opani chinthu chimene chili patsogolo panu ndi pambuyo panu kuti mwina Mulungu angakuonetsereni chifundo” ndipo iwo samvera ayi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذا قيل لهم اتقوا ما بين أيديكم وما خلفكم لعلكم ترحمون, باللغة نيانجا

﴿وإذا قيل لهم اتقوا ما بين أيديكم وما خلفكم لعلكم ترحمون﴾ [يسٓ: 45]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo kukanenedwa kwa iwo: “Opani zomwe ziri patsogolo panu ndi zomwe ziri pambuyo panu kuti muchitiridwe chifundo.” (Iwo akunyoza malangizowo)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek