Quran with Chichewa translation - Surah Ya-Sin ayat 51 - يسٓ - Page - Juz 23
﴿وَنُفِخَ فِي ٱلصُّورِ فَإِذَا هُم مِّنَ ٱلۡأَجۡدَاثِ إِلَىٰ رَبِّهِمۡ يَنسِلُونَ ﴾
[يسٓ: 51]
﴿ونفخ في الصور فإذا هم من الأجداث إلى ربهم ينسلون﴾ [يسٓ: 51]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo lipenga lidzaimbidwa (loukitsa akufa); iwo adzangozindikira akutuluka m’manda kunka kwa Mbuye wawo uku akuthamanga |