×

Ndipo Ife tidaika madalitso athu pa iye ndi pa Isake. Ndipo pakati 37:113 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah As-saffat ⮕ (37:113) ayat 113 in Chichewa

37:113 Surah As-saffat ayat 113 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah As-saffat ayat 113 - الصَّافَات - Page - Juz 23

﴿وَبَٰرَكۡنَا عَلَيۡهِ وَعَلَىٰٓ إِسۡحَٰقَۚ وَمِن ذُرِّيَّتِهِمَا مُحۡسِنٞ وَظَالِمٞ لِّنَفۡسِهِۦ مُبِينٞ ﴾
[الصَّافَات: 113]

Ndipo Ife tidaika madalitso athu pa iye ndi pa Isake. Ndipo pakati pa ana awo pali ena ochita ntchito zabwino ndi ena amene ndi olakwa ndipo amadzipondereza okha

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وباركنا عليه وعلى إسحاق ومن ذريتهما محسن وظالم لنفسه مبين, باللغة نيانجا

﴿وباركنا عليه وعلى إسحاق ومن ذريتهما محسن وظالم لنفسه مبين﴾ [الصَّافَات: 113]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo tidamdalitsa iye ndi (mwana wake) Isihaqa; ndipo m’mbumba ya awiriwa mudapezeka abwino ndi odzichitira zoipa owonekera
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek