Quran with Chichewa translation - Surah As-saffat ayat 22 - الصَّافَات - Page - Juz 23
﴿۞ ٱحۡشُرُواْ ٱلَّذِينَ ظَلَمُواْ وَأَزۡوَٰجَهُمۡ وَمَا كَانُواْ يَعۡبُدُونَ ﴾
[الصَّافَات: 22]
﴿احشروا الذين ظلموا وأزواجهم وما كانوا يعبدون﴾ [الصَّافَات: 22]
Khaled Ibrahim Betala “(Kudzanenedwa kwa angelo): “Asonkhanitseni amene adali osalungama pamodzi ndi akazi awo (okana Allah) ndi milungu yawo imene amaipembedza,” |