Quran with Chichewa translation - Surah As-saffat ayat 51 - الصَّافَات - Page - Juz 23
﴿قَالَ قَآئِلٞ مِّنۡهُمۡ إِنِّي كَانَ لِي قَرِينٞ ﴾
[الصَّافَات: 51]
﴿قال قائل منهم إني كان لي قرين﴾ [الصَّافَات: 51]
Khaled Ibrahim Betala “Adzanena wonena mmodzi wa iwo: “Ine ndidali ndi mnzanga (wopembedza mafano amene amatsutsana nane za chipembedzo ndi zophunzitsa za Qur’an yolemekezeka).” |