Quran with Chichewa translation - Surah sad ayat 42 - صٓ - Page - Juz 23
﴿ٱرۡكُضۡ بِرِجۡلِكَۖ هَٰذَا مُغۡتَسَلُۢ بَارِدٞ وَشَرَابٞ ﴾
[صٓ: 42]
﴿اركض برجلك هذا مغتسل بارد وشراب﴾ [صٓ: 42]
Khaled Ibrahim Betala “(Tidamuyankha kuitana kwake, ndipo tidamuuza): “Menyetsa miyendo yako (panthaka; patuluka madzi) ozizira osamba ndi kumwa (zikuchokera zomwe uli nazo).” |