Quran with Chichewa translation - Surah sad ayat 75 - صٓ - Page - Juz 23
﴿قَالَ يَٰٓإِبۡلِيسُ مَا مَنَعَكَ أَن تَسۡجُدَ لِمَا خَلَقۡتُ بِيَدَيَّۖ أَسۡتَكۡبَرۡتَ أَمۡ كُنتَ مِنَ ٱلۡعَالِينَ ﴾
[صٓ: 75]
﴿قال ياإبليس ما منعك أن تسجد لما خلقت بيدي أستكبرت أم كنت﴾ [صٓ: 75]
Khaled Ibrahim Betala “(Allah) adati: “E iwe Iblis! Nchiyani chakuletsa kugwa pansi ndi kuchilemekeza chimene ndachilenga ndi manja Anga (popanda kutuma wina)? Kodi wadzikweza kapena uli mmodzi wa odziika pamwamba?” |