×

Motero inu pembedzani aliyense amene mufuna kuonjezera pa Mulungu. “Ndithudi otayika ndi 39:15 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zumar ⮕ (39:15) ayat 15 in Chichewa

39:15 Surah Az-Zumar ayat 15 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zumar ayat 15 - الزُّمَر - Page - Juz 23

﴿فَٱعۡبُدُواْ مَا شِئۡتُم مِّن دُونِهِۦۗ قُلۡ إِنَّ ٱلۡخَٰسِرِينَ ٱلَّذِينَ خَسِرُوٓاْ أَنفُسَهُمۡ وَأَهۡلِيهِمۡ يَوۡمَ ٱلۡقِيَٰمَةِۗ أَلَا ذَٰلِكَ هُوَ ٱلۡخُسۡرَانُ ٱلۡمُبِينُ ﴾
[الزُّمَر: 15]

Motero inu pembedzani aliyense amene mufuna kuonjezera pa Mulungu. “Ndithudi otayika ndi iwo amene adzataya miyoyo yawo ndi anthu awo pa tsiku lachiweruzo. Ndithudi kumeneku ndi kutayika kwenikweni.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فاعبدوا ما شئتم من دونه قل إن الخاسرين الذين خسروا أنفسهم وأهليهم, باللغة نيانجا

﴿فاعبدوا ما شئتم من دونه قل إن الخاسرين الذين خسروا أنفسهم وأهليهم﴾ [الزُّمَر: 15]

Khaled Ibrahim Betala
““Choncho pembedzani zimene mwafuna, kumsiya Iye.” Nena (kwa iwo): “Ndithu otaika ndi kuonongeka kwakukulu, ndi amene adzitaya okha, (adziluzitsa okha), ndi maanja awo, patsiku la Qiyâma. Dziwa, ndithu kumeneko ndiko kuluza koonekera.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek