×

Iwo adzakutidwa ndi moto pamwamba pawo ndi magawo a moto pansi pawo. 39:16 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Az-Zumar ⮕ (39:16) ayat 16 in Chichewa

39:16 Surah Az-Zumar ayat 16 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zumar ayat 16 - الزُّمَر - Page - Juz 23

﴿لَهُم مِّن فَوۡقِهِمۡ ظُلَلٞ مِّنَ ٱلنَّارِ وَمِن تَحۡتِهِمۡ ظُلَلٞۚ ذَٰلِكَ يُخَوِّفُ ٱللَّهُ بِهِۦ عِبَادَهُۥۚ يَٰعِبَادِ فَٱتَّقُونِ ﴾
[الزُّمَر: 16]

Iwo adzakutidwa ndi moto pamwamba pawo ndi magawo a moto pansi pawo. Ndi chimenechi; Mulungu amaopseza akapolo ake. “Oh inu akapolo anga motero opani Ine.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: لهم من فوقهم ظلل من النار ومن تحتهم ظلل ذلك يخوف الله, باللغة نيانجا

﴿لهم من فوقهم ظلل من النار ومن تحتهم ظلل ذلك يخوف الله﴾ [الزُّمَر: 16]

Khaled Ibrahim Betala
“Pa iwo padzakhala misanjikosanjiko ya moto ndiponso pansi pawo. Ndi (chilango) chimenechi, Allah akuwaopseza nacho akapolo Ake. “E inu akapolo Anga! Ndiopeni!”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek